08/06/2026
Mwadzuka bwanji?
Tithokonze nonse munatenga nawo gawo.Ndakatulo zolembedwa bwino kwambiri.Koma omwe ndakatulo zawo zapeza ma likes wochuluka ndi awa:
Elijah Chisale 43
Astrepa Bright 37
Kandiero Tunguza 35
Mahajir Umali 19
Aubrey Sally Chikwate 16
Amenewa tiwajambula ndakatulo zimene atipatsazi ndipo tiwathandizira kutumiza ndakatulo zimenezi mma radio
Amene maina Ali apo yakhulani ndi Amfumu Kenneth Khondiwa pa 0997465040