Umodzi Nation

Umodzi Nation BREAKING NEWS
For Entertainment, Education,
Exploring the Country(Malawi),
Sharing thoughts. Connecting People. promoting Music, Movie and Poems.
(2)

25/07/2026

Unachosa mimba ukuvalaso mayala onesa chombo ufuna aone ndani chilizacho

Nde Gym ikumane ndi Bafa kuti khaaa!!
25/07/2026

Nde Gym ikumane ndi Bafa kuti khaaa!!

25/07/2026

Mezan malovu ka 4 mowilikiza ngat mukwanise mulibe edzi

13/07/2026

Muzatifuna chitsikana chikazakuthelani.

29/06/2026

Palibe Chinthu Chowawa Ngt Uzimenyedwa Nde Wina Aziti Asiyeni Musawaleletse😭💔

SAD NEWS🚨🚨Because of poor training management at our police services we have lost this man  Inu intern wapha Munthu 😭😭Fo...
28/06/2026

SAD NEWS🚨🚨

Because of poor training management at our police services we have lost this man

Inu intern wapha Munthu 😭😭
Follow Umodzi Nation for more updates

BREAKING NEWS 📛🔔📣Trump wachenjeza dziko la Iran 🇮🇷 kuti dziko la United States likadali lokonzeka kuchitanso nkhondo nga...
28/06/2026

BREAKING NEWS 📛🔔📣

Trump wachenjeza dziko la Iran 🇮🇷 kuti dziko la United States likadali lokonzeka kuchitanso nkhondo ngati Iran ipitiriza kukulitsa mikangano ya usilikali. Izi zikubwera pambuyo poti asilikali a U.S. achitanso ziwembu zolimbana ndi malo ena a usilikali ku Iran .

Mu uthenga womwe analemba pa Truth Social, Trump adati asilikali a U.S. awononga malo osungirako ma missile ndi ma drone, komanso malo a ma radar m'mphepete mwa nyanja ku Iran. Iye ananena kuti izi zachitika chifukwa cha zomwe adafotokoza kuti ndi kuphwanya mgwirizano wosiya nkhondo (ceasefire) ndi Iran.

Trump anachenjezanso kuti ngati Iran ipitiriza zomwe ikuchitazo, United States "idzakakamizika kumaliza ntchitoyi pogwiritsa ntchito mphamvu za usilikali." Ananenanso kuti, "Dziko la Islamic Republic of Iran silidzakhalaponso."

Follow us for more Umodzi Nation

Address

Dungeness Road, Romney Marsh
Lilongwe
TN299NB

Telephone

+265886448782

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Umodzi Nation posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Umodzi Nation:

Shortcuts

Share