CalmTech

CalmTech secondary tutorials basically in our local language and other computer related tutorials

26/03/2026
26/03/2026

How to improve network strength in our phones

Hello guys it's CalmTech  again,Kodi mumadxiwa kuti M***a kupanga. Combine ma  pdf files ambirimbiri into one file ?Kwa ...
04/03/2026

Hello guys it's CalmTech again,

Kodi mumadxiwa kuti M***a kupanga. Combine ma pdf files ambirimbiri into one file ?

Kwa ma student anxanga this is very helpful make kumapeto Kwa semester ija , kungotenga ma lecture onse kuika kukhala file imodxi Kuma phanda

Omwe tikufuna video kuti tipange , put you comment osaiwala kupanga follow and share .

Thanks 🙏

02/03/2026

how to create another account on your phone

kodi mumadziwa kuti pa phone panupo m***a kukhala ndi ma account opitilira imodxi, ? 🤔🤔🤔kwa anthu omwe mumabwerekana pho...
27/02/2026

kodi mumadziwa kuti pa phone panupo m***a kukhala ndi ma account opitilira imodxi, ? 🤔🤔🤔

kwa anthu omwe mumabwerekana phone aliyense atha kukhala ndi account yake ndipo aliyense kumapanga install ma application ake kukhala ndizochitika zakekumemeko

next video tifotokoza za mene tingapangire zimezi

please follow and like this page

"together we unit divided we fall"

27/02/2026

how to retrieve forgotten password for all websites we logged in before

27/02/2026

how to block p**n sites in our phone

make your phone safe for your children 💞

26/02/2026

how to retrieve forgotten password?

Address

Zomba
Zomba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when CalmTech posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share