Finaltouch

Finaltouch finaltouch IT & Electronics is Malawi's best repair shop for computers and other electronic gadgets.

Ma crack siabho bwerani tizikugulitsani ma license key a original, We uploaded this video on youtube over 3 years ago on...
27/07/2026

Ma crack siabho bwerani tizikugulitsani ma license key a original,

We uploaded this video on youtube over 3 years ago on how to activate windows, pano talandira chisamani kuchokera kwa atchamani.

"Bluetooth is ready to pair", Mau awa musamawamvele kwa neba,Oosagula mtibu wina chifukwa choti Mtibu wanu wanu ulibe Bl...
23/07/2026

"Bluetooth is ready to pair", Mau awa musamawamvele kwa neba,
Oosagula mtibu wina chifukwa choti Mtibu wanu wanu ulibe Bluetooth. Kunopanga plug akaka pa auxi paja basitu kumamvera, nyimbo via bluetooth ,

K25,000 yokha basi ndiye mtengo wake

Lorani kuti ntchito za manja athu zitichitire umboni.Tikunena apayitu ndi MRA. Zambiri tisakambe tikufuna tikavine kaye,...
21/07/2026

Lorani kuti ntchito za manja athu zitichitire umboni.

Tikunena apayitu ndi MRA. Zambiri tisakambe tikufuna tikavine kaye,

Mafunso mutifunse tikabwera k*k

Tima USB card tija timaoneka chonchi, uyu ndi PCI amakhala ndi ma USB Port 4 panja komanso imodzi yamtika. Kumalawi kuno...
16/07/2026

Tima USB card tija timaoneka chonchi, uyu ndi PCI amakhala ndi ma USB Port 4 panja komanso imodzi yamtika.

Kumalawi kuno alipo kale ndipo m***a kugulanso kuchokera kwa ife. Mtengo ndi 35 pin yokha basi .

Gulani online ku website yathu https://ft-mw.com/product/pci-usb-2-0-5-port-expansion-card/

or tipezeni mu Limbe
0981 553 576

Chonena ife tilibe eeeeeeCopied "An MSI customer in Japan paid the company’s service partner, ASK Corporation, to repair...
16/07/2026

Chonena ife tilibe eeeeee

Copied
"An MSI customer in Japan paid the company’s service partner, ASK Corporation, to repair a bent CPU socket pin on their motherboard. However, the board was returned with another pin bent.
After the customer's complaint went viral on X, MSI Japan issued a public apology, pledging to review its repair workflows and address the oversight....."

Ngati mumamva za USB 3.0 koma simumamvetsetsa tamvani izi. Titamufunsa google muchizungu anayankha izi  "USB 3.0 provide...
15/07/2026

Ngati mumamva za USB 3.0 koma simumamvetsetsa tamvani izi. Titamufunsa google muchizungu anayankha izi
"USB 3.0 provides data transfer speeds up to 5 Gbps (10x faster than USB 2.0), delivers increased power (900mA for faster device charging), and features bi-directional communication to send and receive data simultaneously"

Just imagine kutumiza zinthu 10x faster kuposa usb 2.0, izi zimatheka kumagwiritsa ntchito 3.0 USB enclosure .

Ifetu ma enclosure amenewa tili nawo ndipo tikugulitsa.
ma shop athu ali mu Limbe komanso m***a kugula online from our website .

https://ft-mw.com/product/2-5-inch-usb-3-0-hdd-ssd-enclosure/

Kodi mukudziwa kuti m***a kuseva nthawi komanso ndalama mutagula akaka.Mishani iyiyi imapanga convert malo olowa dvd aja...
15/07/2026

Kodi mukudziwa kuti m***a kuseva nthawi komanso ndalama mutagula akaka.

Mishani iyiyi imapanga convert malo olowa dvd aja kuti muzigwiritsa ntchito SATA hardrive/SSD. After all munagwiritsa ntchito DVD/CD ndi liti? you can utilize this opportunity to create room for extra storage.

Izitu ndizabho kwambiri ngati mukufuna kukhala ndi ma SATA drive awiru kapena ngati laptop yanu siimaona ma HDD koma ma DVD imagwira.

Izizi ndizopanda risk, Laptop siingazime coz technician amapanga fix port ya SATA storage. Save your time for other impotant issues man.

14/07/2026

Nkhani yavuta ndi ya AI. Kodi AI ili ndi ubwino wanji ndi field yanu? Eti mukuopa kuti fans ina siiziona phindu chifukwa cha AI?

13/07/2026

Kodi ma software mumapanga download kuti?

tikakhala ife Windows=getintopc.com MAC=oceandmg.com Linux = flahub.org

Address

Livingstone Avenue Limbe
Blantyre
312229

Opening Hours

Monday 08:30 - 17:00
Tuesday 08:30 - 17:00
Wednesday 08:30 - 17:00
Thursday 08:30 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 14:00

Telephone

+265884553576

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Finaltouch posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Finaltouch:

Shortcuts

Share

Category