BrainWave Media

BrainWave Media | Seeing Genius in every Brainwave 🧠 |
For Business,Promo and Adverts
+265 999017065
(2)

04/08/2026

Zilibwino tsopano;
Usiku wabwino

04/08/2026

Munayamba mwamwapo misisi ya chabechabe koma inu mkuzimva kuti mwachila chifukwa cha mankhwala omwe mwamwao?

Nkhani Ija mwainva?😂😂
30/07/2026

Nkhani Ija mwainva?😂😂

Ndayesetsa ma auto tune koma ndivomeleze voice yanga siibwino basi 😂😂 Ndikakhala bho video ibwera ma guy osaopa.
30/07/2026

Ndayesetsa ma auto tune koma ndivomeleze voice yanga siibwino basi 😂😂
Ndikakhala bho video ibwera ma guy osaopa.

Nde Mutawafunsa akuti amamanga cholemberacho chifukwa chani? Mwina timaoneka okaikitsa 😂😂😂
29/07/2026

Nde Mutawafunsa akuti amamanga cholemberacho chifukwa chani?
Mwina timaoneka okaikitsa 😂😂😂

27/07/2026

Kodi eti N'chifukwa chani simuganiza zochoka ku Malawi? 🇲🇼

24/07/2026

Kodi Munamvapo za Survivorship bias?

Success ya ena isakupatseni pressure, ingokhalani mu lane yanu pa Speed yanu. BrainWave Media
22/07/2026

Success ya ena isakupatseni pressure, ingokhalani mu lane yanu pa Speed yanu. BrainWave Media

Lero lokha akuluakulu ndiyamikireni 😂😂. Mwina GOAT wanga akakanika kutenga Chinthuchi usiku uno, ndikhala mwezi osaponya...
19/07/2026

Lero lokha akuluakulu ndiyamikireni 😂😂. Mwina GOAT wanga akakanika kutenga Chinthuchi usiku uno, ndikhala mwezi osaponya video.akudziwa ndani?

18/07/2026

Kodi Munayamba mwamvapo za Decoy Effect?

Address

Capetown
Lilongwe

Telephone

+265995371612

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when BrainWave Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to BrainWave Media:

Shortcuts

Share